Comments (0)

Kufotokoza mwachidule ntchito zathu ku Malawi

Mgwirizano wa Zurich Flood Resilience Alliance ndi mgwirizano wamagawo ambiri umene umafufuza njira zothandiza madera aku mayiko otukuka komanso amene akutukuka kuti alimbikitse kupilira kwawo pachiwopsezo cha kusefukira kwamadzi. Bungwe la Concern Worldwide lakhala likugwira ntchito ku Malawi kuyambira m’chaka cha 2002, ndipo lili ndi mbiri yabwino kwambiri pokonza ndondomeko komanso utsogoleri wamphamvu pamaudindo opezera ndalama, kuteteza anthu, kulimbikitsa amayi, kadyedwe koyenera, komanso kuthandiza anthu panthawi ya ngozi.
Author: Concern Worldwide
Language: Other
Pubished By: The Zurich Flood Resilience Alliance
Pubished date: September 2021

Post a comment

Your email address will not be published. Required fields are marked *


Comments

Do you have any question?